Kodi mukudziwa kuti moyo wa munthu padziko lapansi ndi nkhondo? Tili pankhondo kaya tasankha kukhala pankhondo kapena ayi. Baibulo limati moyo wanu ndi nkhondo. Inu muyenera kumenya nkhondo yabwino ndi kupambana nkhondoyo. Bukhu latsopanoli pa nkhondo ndiloyenera kuwerengedwa ndi atsogoleri.