Mukusirira kukhala odzozedwa? Mu bukhu la mbiri ili, Dr. Heward-Mills akugawana nafe ndondomeko zolandirira kudzoza. Bukhuli likakhala maka maka mdalitso kwa inu ndi utumiki wanu. Zindikirani ndondomeko mukufunikira kutenga kuti mukhale odzozedwa!