Baibulo limatitululira Mpingo wa Chipangano Chatsopano umene unadzazidwa ndi miyoyo ya masauzande ambiri. Pamene mpingo uli ndi miyoyo ya masauzande ambiri, umatchedwa mpingo waukulu, kapena Mega Church. Ngati Mulungu wayika m'mtima mwanu masomphenya omanga mpingo waukulu wa mtundu uwu, bukuli ndilo lidzakuthandizani kukwaniritsa loto limenelo. Wolemba bukuli, Dag Heward-Mills, m'bukuli lodabwitsali akufotokoza chifukwa chake mdierekezi amatsutsa kusonkhana kwa mpingo, komanso akuwonetsa mmene sitepe zosavuta za kubzala mipingo iing'onoing'ono 1000 ngati mbeu (micro churches) zingakuthandizireni kumanga Mega Church.
Utumiki wanu usinthe kwambiri kudzera mu mphamvu zamphamvu za mipingo iing'onoing'ono 1000 imeneyi!